Trap Squad - Ngati Mzimbe lyrics

Published

0 77 0

Trap Squad - Ngati Mzimbe lyrics

Intro [Revolver] Trap squad aise Royal fam Yeah Verse 1 [revolver] Zimakoma kumathelo ngati bus ya kwa jali Nkhawa utapanga burry ngati braz ya patali Chapatali timakhala ngati tapenga Mkazi wanga wa mmaloto uja ndampeza Akandinong'oneza zam'dziko ndimapanga mute Amvekele my crooked smile is kinda cute Unali kuti moyo wanga wonseu You make a G turn soft when you say you-gotta go Ati kwada is the reason Ndinamuwuza usapite ngati chisoni Baby you're the cure to my disease Mtima wanga umandipweteka when you leave Gave you my heart do with it as you please I wish I could take this moment and freeze Usakaike ndiwe wanga basi Ndikamatchila ndi iwe zimakhala ngati Mzimbe Chorus [sir patricks, stich fray] Ngati mzimbe ukomela ku msinde Ngati tulo likoma ku mbanda kucha Tikamacheza usapite honey usapite Tikamacheza ngati usapite honey usapite tizicheza Verse 2 [Chavura] Sweet ndingofila bho man Ndavaya kwao wandishophela ka yogurt Which ndingomwela stroll man Wa awuza ana panja kuti chokani Muti sokoneza Muti phokosela Ndamugwila nkhosi easy kumunong'oneza Wandipasa kiss ngati barabas Mkazi uyu ine ndimupasa mwana basi Mkulu wina anamdyesa nazo nyani Atakomedwa kutchatisa ka mkazi Anachita kufasa kukombezela msuzi Osadziwa kuti akudya barboon Me anandiuza I love you Ndakuphikila zokoma iwe top goon Nnamupasa kaye mphaka alawe portion Sukudziwa mwina mfana wathila poison (back to chorus) Verse 3 [sir patricks] Umalasa mtima ukatulukila Ukati honey ndabwela kuzakuphikila Pachisoni kachikondi amazembelera Poti ndimadziwa wabwela za temporaly posachedwa usanzika [stich fray] Mutu wanga umazungulira Zimandivuta mtimawu kuwugwila ine Ndikakuona iwe ukupita Mu mtima mumawawa mutu umawawa Kuganizila zina Sizitheka ndipo sindimaona mdima Tingokwatila mwina Its hard to watch you go ndipo zili ngati mzimbe