Eminent Boiz - Dosage lyrics

Published

0 183 0

Eminent Boiz - Dosage lyrics

Verse 1 Kungodzuka mawa mami kufuna. ntakuonaaa Nkona ndimabwera kwanu kusanache utha kuona Chomwe ndimafuna Mami wekha sukudziwa Koma chomwe ndimafuna mami ndekha ndimadziwa Ndimataya ntima koma iwe sunditola Kukusowa sindingathe poti nthawi sindilora Tidadyetsana chani fanzi ati imangodabwa Tima yoh tikakuyesa. tokhaso. kumangodabwa Unaonamo. Mpaka lero simmadziwa Ndilibe kalikose orso UNIMA anandisiya Dosage yanga ndiwe sindi funa kukumisa Ena akuti overdose mu chikondi unandimiza CHORUS(HOOK) Iiineyooo Kukhala opanda iwe sindigathe mami Ndiwe doSage yanga Umafunika nthawi yoyenerera Without U sindimava bwino ineeeE Ndiwe dossage yanga* X4 M'mawa masana madzulo ndiwe babie Verse 2 Iweyo NDE kanyale sinkuthira madzi or manyowa Zonse Unganena ndiku Mvera ngati Duwa Ndilibe ntima mami ndiwe amene Nakupatsa Ukatalikira ndimadanda ndekha ntangofatsa Ndi. Dzafusira mbeta adzandirore kwanu komwe Nsidzaopa kamulako ngati zamlomwe Mawa masana Madzulo mami umafunikiraaa Opanda iwe nditha kufa Osamwinikila Ati Chikondi pa chikondi imakhala nkhani ina Nde Abatiya pa iweyo amapanga nkhani ina Dosage yanga ndiwe sindi funa kukumisa Ena akuti overdose mu chikondi unandimiza BACK TO HOOK Verse 3 Ati swagg imandivuta ndinakhoza mpaka fail Kodi tizinchonchonana? kukhala samatero Amanena zambiri anthuwa ndimawamva Koma sindiwatengera amavutika muntima Ineyo opanda iwe na moyo umavuta Ndiwe wanga wanga lady Pamaso pa chauta Dosage yokwanira sindipanga overdose Ndikapanda kukuona ndimathakugwetsa Nsozi Pamavuto pa ntendere mami Umafunikira Opanda iwe nditha kufa Osapenekera Dosage yanga ndiwe sindi funa kukumisa Ena akuti overdose muchikondi unandimiza